Levitiko 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu aliyense mwa ana a Aroni wansembe, amene ali ndi chilema, asayandikire guwa lansembe kudzapereka nsembe yotentha ndi moto kwa Yehova.+ Iye ali ndi chilema. Asayandikire guwa lansembe kudzapereka mkate wa Mulungu wake.+
21 Munthu aliyense mwa ana a Aroni wansembe, amene ali ndi chilema, asayandikire guwa lansembe kudzapereka nsembe yotentha ndi moto kwa Yehova.+ Iye ali ndi chilema. Asayandikire guwa lansembe kudzapereka mkate wa Mulungu wake.+