Numeri 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuchokera ku fuko la Nafitali,+ Ahira+ mwana wa Enani. Numeri 7:78 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 78 Pa tsiku la 12 panali mtsogoleri wa ana a Nafitali, Ahira+ mwana wa Enani. Numeri 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipo mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Nafitali+ anali Ahira,+ mwana wa Enani.