Genesis 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Rakele anati: “Ndalimbana mwamphamvu ndi m’bale wanga ndipo ndapambananso.” Chotero anatcha mwanayo dzina lakuti Nafitali.*+ Genesis 49:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Nafitali+ ndi mbawala yaikazi yopepuka miyendo, ndipo amanena mawu okoma.+
8 Ndiyeno Rakele anati: “Ndalimbana mwamphamvu ndi m’bale wanga ndipo ndapambananso.” Chotero anatcha mwanayo dzina lakuti Nafitali.*+