Deuteronomo 33:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo kwa Nafitali anati:+“Nafitali wakhutira chifukwa chovomerezedwa ndi Yehova,Ndipo madalitso Ake amuchulukira.Tenga chigawo cha kumadzulo ndi kum’mwera.”+ Yoswa 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Maere a 6+ anagwera ana a Nafitali+ potsata mabanja awo. Mateyu 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Anthu okhala m’dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafitali, m’mbali mwa msewu wa kunyanja kutsidya lina la Yorodano, ku Galileya+ kumene kunali kukhala anthu a mitundu ina,
23 Ndipo kwa Nafitali anati:+“Nafitali wakhutira chifukwa chovomerezedwa ndi Yehova,Ndipo madalitso Ake amuchulukira.Tenga chigawo cha kumadzulo ndi kum’mwera.”+
15 “Anthu okhala m’dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafitali, m’mbali mwa msewu wa kunyanja kutsidya lina la Yorodano, ku Galileya+ kumene kunali kukhala anthu a mitundu ina,