Deuteronomo 33:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo kwa Nafitali anati:+“Nafitali wakhutira chifukwa chovomerezedwa ndi Yehova,Ndipo madalitso Ake amuchulukira.Tenga chigawo cha kumadzulo ndi kum’mwera.”+
23 Ndipo kwa Nafitali anati:+“Nafitali wakhutira chifukwa chovomerezedwa ndi Yehova,Ndipo madalitso Ake amuchulukira.Tenga chigawo cha kumadzulo ndi kum’mwera.”+