Deuteronomo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Pa nthawi imeneyo tinalanda dziko m’manja mwa mafumu awiri amenewo a Aamori+ amene anali kukhala m’dera la Yorodano, kuyambira m’chigwa* cha Arinoni+ mpaka kuphiri la Herimoni.+
8 “Pa nthawi imeneyo tinalanda dziko m’manja mwa mafumu awiri amenewo a Aamori+ amene anali kukhala m’dera la Yorodano, kuyambira m’chigwa* cha Arinoni+ mpaka kuphiri la Herimoni.+