Numeri 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choka! Nyamuka uzipita. Ine ndimati ndikupatse ulemerero,+ koma taona! Yehova wakumanitsa ulemererowo.” Miyambo 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Woipa amatenga chiphuphu mobisa,+ kuti akhotetse njira za chiweruzo.+
11 Choka! Nyamuka uzipita. Ine ndimati ndikupatse ulemerero,+ koma taona! Yehova wakumanitsa ulemererowo.”