Numeri 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndithu ndidzakupatsani ulemerero waukulu,+ ndipo chilichonse chimene mungandiuze ndidzachita.+ Chonde tabwerani mudzanditembererere anthuwa.’” Yuda 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+
17 Ndithu ndidzakupatsani ulemerero waukulu,+ ndipo chilichonse chimene mungandiuze ndidzachita.+ Chonde tabwerani mudzanditembererere anthuwa.’”
11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+