13 ‘Ngakhale Balaki atandipatsa nyumba yake yodzaza siliva ndi golide, sindingachite chochokera mumtima mwanga, kaya chabwino kapena choipa, chosemphana ndi zimene Yehova walamula? Sindinanene kodi, kuti chilichonse chimene Yehova ati alankhule, ndilankhula chomwecho’?+