Numeri 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Balamu anayankha atumiki a Balaki aja kuti: “Ngakhale Balaki atandipatsa nyumba yake yodzaza siliva ndi golide, sindingachite chilichonse mosemphana ndi zimene Yehova Mulungu wanga angandilamule, kaya kuchotsera kapena kuwonjezerapo.+ Numeri 22:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Balamu anayankha Balaki kuti: “Si ine ndabwerane! Inetu sindingathe kunena kalikonse.+ Mawu amene Yehova ati aike m’kamwa mwangamu ndi amene ndilankhule.”+
18 Koma Balamu anayankha atumiki a Balaki aja kuti: “Ngakhale Balaki atandipatsa nyumba yake yodzaza siliva ndi golide, sindingachite chilichonse mosemphana ndi zimene Yehova Mulungu wanga angandilamule, kaya kuchotsera kapena kuwonjezerapo.+
38 Balamu anayankha Balaki kuti: “Si ine ndabwerane! Inetu sindingathe kunena kalikonse.+ Mawu amene Yehova ati aike m’kamwa mwangamu ndi amene ndilankhule.”+