Numeri 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Balamu atamva mawuwo anawawuza kuti: “Gonani konkuno lero. Ndikuyankhani malinga n’zimene Yehova ati andiuze.”+ Akalonga a ku Mowabuwo anagonadi kwa Balamu.
8 Balamu atamva mawuwo anawawuza kuti: “Gonani konkuno lero. Ndikuyankhani malinga n’zimene Yehova ati andiuze.”+ Akalonga a ku Mowabuwo anagonadi kwa Balamu.