Numeri 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawauza kuti: “Mvetserani mawu anga. Pakanakhala mneneri wa Yehova pakati panu, ndikanamudziwitsa za ine m’masomphenya,+ ndipo ndikanalankhula naye m’maloto.+ Numeri 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iye anamuyankha kuti: “Kodi chilichonse chimene Yehova wandiika m’kamwa, si chimene ndinayenera kunena?”+
6 Iye anawauza kuti: “Mvetserani mawu anga. Pakanakhala mneneri wa Yehova pakati panu, ndikanamudziwitsa za ine m’masomphenya,+ ndipo ndikanalankhula naye m’maloto.+
12 Koma iye anamuyankha kuti: “Kodi chilichonse chimene Yehova wandiika m’kamwa, si chimene ndinayenera kunena?”+