Numeri 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero anamutengera ku Zofimu, pamwamba pa phiri la Pisiga.+ Kumeneko anamanga maguwa ansembe 7, n’kupereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+ Numeri 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero Balaki anachita monga momwe Balamu ananenera. Anapereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+
14 Chotero anamutengera ku Zofimu, pamwamba pa phiri la Pisiga.+ Kumeneko anamanga maguwa ansembe 7, n’kupereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+
30 Chotero Balaki anachita monga momwe Balamu ananenera. Anapereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+