Numeri 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano Balamu anauza Balaki kuti: “Mundimangire pamalo ano maguwa ansembe+ okwanira 7. Mukatero mundikonzere ng’ombe zamphongo 7, ndi nkhosa zamphongo 7.” Numeri 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kumeneko Balamu+ anauza Balaki kuti: “Mundimangire pamalo ano maguwa ansembe 7, ndipo mundikonzere ng’ombe zamphongo 7, ndi nkhosa zamphongo 7.”+
23 Tsopano Balamu anauza Balaki kuti: “Mundimangire pamalo ano maguwa ansembe+ okwanira 7. Mukatero mundikonzere ng’ombe zamphongo 7, ndi nkhosa zamphongo 7.”
29 Kumeneko Balamu+ anauza Balaki kuti: “Mundimangire pamalo ano maguwa ansembe 7, ndipo mundikonzere ng’ombe zamphongo 7, ndi nkhosa zamphongo 7.”+