Numeri 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 M’mawa kutacha, Balaki anakatenga Balamu n’kupita naye ku Bamoti-baala.+ Anam’tengera kumeneko kuti akathe kuliona bwino khamu lonse la Aisiraeli.+
41 M’mawa kutacha, Balaki anakatenga Balamu n’kupita naye ku Bamoti-baala.+ Anam’tengera kumeneko kuti akathe kuliona bwino khamu lonse la Aisiraeli.+