Numeri 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno Balaki anauza Balamu kuti: “Tabwerani chonde, tiyeni tipite kumalo ena kumene mungathe kuwaona anthuwo. Simukaona onse, koma mukangoona okhawo amene ali chakufupi.+ Mukanditembererere amenewo.”+
13 Ndiyeno Balaki anauza Balamu kuti: “Tabwerani chonde, tiyeni tipite kumalo ena kumene mungathe kuwaona anthuwo. Simukaona onse, koma mukangoona okhawo amene ali chakufupi.+ Mukanditembererere amenewo.”+