Numeri 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ‘Taonani! Anthu amene achokera ku Iguputo adzaza dziko lino kulikonse kumene munthu angayang’ane.+ Tsopano bwerani, mudzanditembererere anthuwa,+ kuti mwina ndingathe kumenyana nawo n’kuwathamangitsa.’”
11 ‘Taonani! Anthu amene achokera ku Iguputo adzaza dziko lino kulikonse kumene munthu angayang’ane.+ Tsopano bwerani, mudzanditembererere anthuwa,+ kuti mwina ndingathe kumenyana nawo n’kuwathamangitsa.’”