Numeri 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ‘Taonani! Anthu amene achokera ku Iguputo aja adzaza dziko lonse lapansi kumene munthu angayangʼane. Tsopano bwerani, mudzatemberere anthuwa.+ Mwina ndingathe kumenyana nawo nʼkuwathamangitsa.’”
11 ‘Taonani! Anthu amene achokera ku Iguputo aja adzaza dziko lonse lapansi kumene munthu angayangʼane. Tsopano bwerani, mudzatemberere anthuwa.+ Mwina ndingathe kumenyana nawo nʼkuwathamangitsa.’”