-
Numeri 22:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Tsopano iye anatumiza amithenga kwa Balamu,+ mwana wa Beori, ku Petori+ pafupi ndi Mtsinje*+ wa m’dziko lawo. Anawatuma kuti akamuitane, kuti: “Taonani! Anthu ochokera ku Iguputo afika kuno. Iwo adzaza dziko lino kulikonse kumene munthu angayang’ane,+ ndipo akukhala pafupi penipeni moyang’anana ndi ine.
-