Numeri 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mʼmawa kutacha, Balaki anakatenga Balamu nʼkupita naye ku Bamoti-baala. Anapita naye kumeneko kuti akathe kuliona bwino gulu lonse la Aisiraeli.+
41 Mʼmawa kutacha, Balaki anakatenga Balamu nʼkupita naye ku Bamoti-baala. Anapita naye kumeneko kuti akathe kuliona bwino gulu lonse la Aisiraeli.+