Ekisodo 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo Eleazara mwana wa Aroni,+ anatenga mwana wamkazi wa Putieli kukhala mkazi wake. Ndipo iye anam’berekera Pinihasi.+ Amenewa ndiwo atsogoleri a mabanja a m’fuko la Levi, malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+ Deuteronomo 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Pamenepo ana a Isiraeli ananyamuka kuchoka ku Beeroti Bene-yaakana+ kupita ku Mosera. Aroni anafera kumalo amenewo, ndipo anamuikanso kumeneko.+ Mwana wake Eleazara anayamba kutumikira monga wansembe m’malo mwa Aroniyo.+
25 Ndipo Eleazara mwana wa Aroni,+ anatenga mwana wamkazi wa Putieli kukhala mkazi wake. Ndipo iye anam’berekera Pinihasi.+ Amenewa ndiwo atsogoleri a mabanja a m’fuko la Levi, malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+
6 “Pamenepo ana a Isiraeli ananyamuka kuchoka ku Beeroti Bene-yaakana+ kupita ku Mosera. Aroni anafera kumalo amenewo, ndipo anamuikanso kumeneko.+ Mwana wake Eleazara anayamba kutumikira monga wansembe m’malo mwa Aroniyo.+