Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 20:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Tsopano Yehova analankhula ndi Mose ndi Aroni m’phiri la Hora, m’malire a dziko la Edomu, kuti:

  • Numeri 20:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Aroni aikidwe m’manda, agone ndi makolo ake,+ pakuti sadzalowa m’dziko limene ndidzapatse ana a Isiraeli. Izi zili choncho chifukwa amuna inu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+

  • Numeri 33:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Wansembe Aroni anakwera m’phiri la Hora monga mmene Yehova anamulamulira, ndipo anamwalira ali m’phirimo. Anamwalira m’chaka cha 40 kuchokera pamene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo, m’mwezi wachisanu, pa tsiku loyamba la mweziwo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena