Salimo 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+ Salimo 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,Makolo athu anatifotokozera+Ntchito zimene inu munachita m’masiku awo,+M’masiku akale.+ Salimo 126:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova watichitira zazikulu.+Tasangalala.+ Aroma 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?
19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+
44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,Makolo athu anatifotokozera+Ntchito zimene inu munachita m’masiku awo,+M’masiku akale.+
33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?