Numeri 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ana a Isiraeli azikhoma mahema awo, aliyense azikhoma hema wake m’chigawo chawo cha mafuko atatu,+ potsata chizindikiro cha nyumba ya makolo ake. Azikhoma mahema awo mozungulira chihema chokumanako komanso moyang’ana chihemacho. Numeri 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti pomwe ndili pano ndikutha kuwaona, pamwamba pa matanthwe pano,Ndikuwaona ndithu, pano pamwamba pa mapiri.Akukhala paokhaokha m’mahema awo,+Iwo akudziona kuti ndi osiyana ndi mitundu ina.+
2 “Ana a Isiraeli azikhoma mahema awo, aliyense azikhoma hema wake m’chigawo chawo cha mafuko atatu,+ potsata chizindikiro cha nyumba ya makolo ake. Azikhoma mahema awo mozungulira chihema chokumanako komanso moyang’ana chihemacho.
9 Pakuti pomwe ndili pano ndikutha kuwaona, pamwamba pa matanthwe pano,Ndikuwaona ndithu, pano pamwamba pa mapiri.Akukhala paokhaokha m’mahema awo,+Iwo akudziona kuti ndi osiyana ndi mitundu ina.+