Numeri 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 “Ana a Isiraeli azimanga mahema awo, aliyense malinga ndi msasa wawo, munthu aliyense malinga ndi gulu lake la mafuko atatu,+ malinga ndi magulu awo a asilikali. Numeri 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene Balamu anakweza maso ake n’kuona Aisiraeli ali m’misasa mwa mafuko awo,+ mzimu wa Mulungu unafika pa iye.+
52 “Ana a Isiraeli azimanga mahema awo, aliyense malinga ndi msasa wawo, munthu aliyense malinga ndi gulu lake la mafuko atatu,+ malinga ndi magulu awo a asilikali.
2 Pamene Balamu anakweza maso ake n’kuona Aisiraeli ali m’misasa mwa mafuko awo,+ mzimu wa Mulungu unafika pa iye.+