Numeri 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Balamu anayamba kulankhula mwa ndakatulo,+ kuti:“Balaki mfumu ya Mowabu yandiitana kuchokera ku Aramu,+Kuchokera kumapiri a kum’mawa, kuti:‘Bwera, udzanditembererere Yakobo.Bwera, udzaitanire tsoka pa Isiraeli.’+
7 Pamenepo Balamu anayamba kulankhula mwa ndakatulo,+ kuti:“Balaki mfumu ya Mowabu yandiitana kuchokera ku Aramu,+Kuchokera kumapiri a kum’mawa, kuti:‘Bwera, udzanditembererere Yakobo.Bwera, udzaitanire tsoka pa Isiraeli.’+