Numeri 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo Balamu anayambanso kulankhula mwa ndakatulo, kuti:+“Nyamuka, Balaki iwe, tamvera.Tchera khutu kwa ine, iwe mwana wa Zipori.+ Numeri 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anayamba kulankhula mwa ndakatulo,+ kuti: “Mawu a Balamu mwana wa Beori,Mawu a mwamuna wamphamvu, maso ake ali chitsegukire,+
18 Pamenepo Balamu anayambanso kulankhula mwa ndakatulo, kuti:+“Nyamuka, Balaki iwe, tamvera.Tchera khutu kwa ine, iwe mwana wa Zipori.+
3 Pamenepo anayamba kulankhula mwa ndakatulo,+ kuti: “Mawu a Balamu mwana wa Beori,Mawu a mwamuna wamphamvu, maso ake ali chitsegukire,+