Levitiko 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Nadabu ndi Abihu,+ ana a Aroni, aliyense anatenga chofukizira,+ n’kuikamo moto ndi zofukiza+ pamwamba pake. Pamenepo anayamba kupereka zofukiza pamoto wosaloledwa+ ndi Yehova, umene iye sanawalamule. Numeri 26:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Koma Nadabu ndi Abihu anafa chifukwa chofukiza moto wosaloleka pamaso pa Yehova.+
10 Ndiyeno Nadabu ndi Abihu,+ ana a Aroni, aliyense anatenga chofukizira,+ n’kuikamo moto ndi zofukiza+ pamwamba pake. Pamenepo anayamba kupereka zofukiza pamoto wosaloledwa+ ndi Yehova, umene iye sanawalamule.