Ekisodo 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aroni anatenga Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wake wa Naasoni,+ kukhala mkazi wake. Ndipo Eliseba anam’berekera Nadabu, Abihu, Eleazara ndi Itamara.+ 1 Mbiri 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nadabu ndi Abihu+ anamwalira opanda ana aamuna bambo awo akali ndi moyo,+ koma Eleazara+ ndi Itamara anapitiriza kukhala ansembe.
23 Aroni anatenga Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wake wa Naasoni,+ kukhala mkazi wake. Ndipo Eliseba anam’berekera Nadabu, Abihu, Eleazara ndi Itamara.+
2 Nadabu ndi Abihu+ anamwalira opanda ana aamuna bambo awo akali ndi moyo,+ koma Eleazara+ ndi Itamara anapitiriza kukhala ansembe.