Numeri 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndiye anali kuyang’anira onse otumikira pamalo oyera. Numeri 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’phirimo, ukamuvule Aroni zovala zake zaunsembe,+ n’kuveka mwana wake Eleazara.+ Aroni akamwalira kumeneko n’kugona ndi makolo ake.”+
32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndiye anali kuyang’anira onse otumikira pamalo oyera.
26 M’phirimo, ukamuvule Aroni zovala zake zaunsembe,+ n’kuveka mwana wake Eleazara.+ Aroni akamwalira kumeneko n’kugona ndi makolo ake.”+