Numeri 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Eleazara mwana wa wansembe Aroni, aziyang’anira+ mafuta+ a nyale, zofukiza zonunkhira,+ nsembe yanthawi zonse yambewu,+ ndi mafuta odzozera.+ Aziyang’aniranso chihema chonse chopatulika ndi zonse za mmenemo, ndiwo malo oyerawo ndi ziwiya zake.” Numeri 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe n’kuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika m’phirimo.
16 “Eleazara mwana wa wansembe Aroni, aziyang’anira+ mafuta+ a nyale, zofukiza zonunkhira,+ nsembe yanthawi zonse yambewu,+ ndi mafuta odzozera.+ Aziyang’aniranso chihema chonse chopatulika ndi zonse za mmenemo, ndiwo malo oyerawo ndi ziwiya zake.”
28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe n’kuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika m’phirimo.