Ekisodo 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako utenge mafuta odzozera+ ndi kuwathira pamutu pake ndi kum’dzoza.+ Ekisodo 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Koma iweyo utenge mafuta awa onunkhira, abwino koposa:+ madontho oundana a mule*+ masekeli 500, sinamoni*+ wonunkhira bwino hafu ya muyezo wa mule, kapena kuti masekeli 250, ndi kalamasi* wonunkhira+ wokwana masekeli 250. Levitiko 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pomalizira, Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni ndi kum’dzoza kuti akhale wopatulika.+ Salimo 133:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu,+Amene akutsikira kundevu,Ndevu za Aroni,+Amenenso akuyenderera mpaka m’khosi la zovala zake.+
23 “Koma iweyo utenge mafuta awa onunkhira, abwino koposa:+ madontho oundana a mule*+ masekeli 500, sinamoni*+ wonunkhira bwino hafu ya muyezo wa mule, kapena kuti masekeli 250, ndi kalamasi* wonunkhira+ wokwana masekeli 250.
12 Pomalizira, Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni ndi kum’dzoza kuti akhale wopatulika.+
2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu,+Amene akutsikira kundevu,Ndevu za Aroni,+Amenenso akuyenderera mpaka m’khosi la zovala zake.+