Ekisodo 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako utenge mafuta odzozera+ nʼkuwathira pamutu pake kuti akhale wodzozedwa.+