Ekisodo 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Samala ndipo umvere mawu ake. Usam’pandukire, chifukwa sadzalekerera zolakwa zanu,+ pakuti dzina langa lili mwa iye. Salimo 106:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pinihasi ataimirira ndi kuchitapo kanthu,+Mliriwo unatha.
21 Samala ndipo umvere mawu ake. Usam’pandukire, chifukwa sadzalekerera zolakwa zanu,+ pakuti dzina langa lili mwa iye.