Numeri 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Pinihasi+ mwana wa Eleazara, mdzukulu wa wansembe Aroni, ataona zimenezi nthawi yomweyo ananyamuka pakati pa khamulo n’kutenga mkondo waung’ono m’dzanja lake.
7 Koma Pinihasi+ mwana wa Eleazara, mdzukulu wa wansembe Aroni, ataona zimenezi nthawi yomweyo ananyamuka pakati pa khamulo n’kutenga mkondo waung’ono m’dzanja lake.