Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 6:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndipo Eleazara mwana wa Aroni,+ anatenga mwana wamkazi wa Putieli kukhala mkazi wake. Ndipo iye anam’berekera Pinihasi.+

      Amenewa ndiwo atsogoleri a mabanja a m’fuko la Levi, malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+

  • Yoswa 22:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Wansembe Pinihasi,+ atsogoleri a khamu la Aisiraeli+ kapena kuti atsogoleri a masauzande a Aisiraeli amene anali naye, atamva mawu amene ana a Rubeni, ana a Gadi ndi ana a Manase ananena, anakhutira nawo mawuwo.

  • 1 Mbiri 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Eleazara+ anabereka Pinihasi,+ Pinihasi anabereka Abisuwa,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena