Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 25:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Pinihasi+ mwana wa Eleazara, mdzukulu wa wansembe Aroni, wabweza mkwiyo wanga+ pa ana a Isiraeli, chifukwa sanalekerere konse zoti anthu azipikisana nane pakati pawo.+ Inetu ndikanawafafanizadi ana a Isiraeliwa, chifukwa ndimafuna kuti azikhala odzipereka kwa ine ndekha basi.+

  • 1 Mbiri 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pinihasi+ mwana wa Eleazara+ ndiye anali mtsogoleri wawo kalekale, ndipo Yehova anali naye.+

  • Salimo 106:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Pinihasi ataimirira ndi kuchitapo kanthu,+

      Mliriwo unatha.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena