11 “Pinihasi+ mwana wa Eleazara, mdzukulu wa wansembe Aroni, wabweza mkwiyo wanga pa Aisiraeli, chifukwa sanalekerere ngakhale pangʼono kuti anthu azipikisana nane pakati pawo.+ Choncho sindinawononge Aisiraeliwa, ngakhale kuti ndimafuna kuti anthu azikhala odzipereka kwa ine ndekha.+