Numeri 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Likhale pangano la unsembe kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale,+ chifukwa sanalekerere zoti anthu azipikisana ndi Mulungu wake,+ ndiponso waphimba machimo a ana a Isiraeli.’”+ Machitidwe 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+
13 Likhale pangano la unsembe kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale,+ chifukwa sanalekerere zoti anthu azipikisana ndi Mulungu wake,+ ndiponso waphimba machimo a ana a Isiraeli.’”+
9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+