Numeri 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uwabwezere+ Amidiyani+ pa zimene anachitira ana a Isiraeli. Pambuyo pake udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.”+
2 “Uwabwezere+ Amidiyani+ pa zimene anachitira ana a Isiraeli. Pambuyo pake udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.”+