Ekisodo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Awa ndi mayina a ana aamuna a Levi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo:+ Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Ndipo Levi anakhala ndi moyo zaka 137. 1 Mbiri 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Levi+ anali Gerisoni,+ Kohati,+ ndi Merari.+
16 Awa ndi mayina a ana aamuna a Levi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo:+ Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Ndipo Levi anakhala ndi moyo zaka 137.