Ekisodo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo ana a Kohati anali Amuramu, Izara, Heburoni ndi Uziyeli.+ Kohati anakhala ndi moyo zaka 133. Numeri 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mwa ana a Kohati, panali banja la Aamuramu, banja la Aizara, banja la Aheburoni ndi banja la Auziyeli. Awa ndiwo anali mabanja a Akohati.+
18 Ndipo ana a Kohati anali Amuramu, Izara, Heburoni ndi Uziyeli.+ Kohati anakhala ndi moyo zaka 133.
27 Mwa ana a Kohati, panali banja la Aamuramu, banja la Aizara, banja la Aheburoni ndi banja la Auziyeli. Awa ndiwo anali mabanja a Akohati.+