33 Koma Tselofekadi, mwana wamwamuna wa Heferi, analibe ana aamuna koma aakazi okhaokha.+ Mayina a ana aakazi a Tselofekadi anali: Mala, Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.+
15 Makiri anapezera akazi Hupimu ndi Supimu, ndipo dzina la mlongo wake linali Maaka.) Mwana wake wachiwiri dzina lake linali Tselofekadi,+ koma Tselofekadi anali ndi ana aakazi okhaokha.+