Yoswa 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tselofekadi+ mwana wa Heferi, mwana wa Giliyadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, analibe ana aamuna, koma anali ndi ana aakazi. Mayina a anawo anali: Mala, Nowa, Hogila, Milika, ndi Tiriza.+
3 Tselofekadi+ mwana wa Heferi, mwana wa Giliyadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, analibe ana aamuna, koma anali ndi ana aakazi. Mayina a anawo anali: Mala, Nowa, Hogila, Milika, ndi Tiriza.+