Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 16:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Dziwani kuti Yehova wakupatsani sabata.+ N’chifukwa chake akukupatsani mkate wa masiku awiri pa tsiku la 6. Pa tsiku la 7 aliyense azikhala pamalo ake.+ Munthu asachoke pamalo ake.”

  • Ekisodo 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma tsiku la 7 ndi sabata la Yehova Mulungu wanu.+ Musagwire ntchito iliyonse inuyo kapena mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, chiweto chanu kapena mlendo wokhala mumzinda wanu.+

  • Ezekieli 20:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndinawapatsanso sabata langa+ kuti likhale chizindikiro pakati pa ine ndi iwowo.+ Ndinachita zimenezi n’cholinga choti adziwe kuti ine Yehova, ndiye amene ndikuwapatula.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena