Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pa tsiku loyamba muzidzachita msonkhano wopatulika, ndipo pa tsiku la 7 muzidzachitanso msonkhano wopatulika.+ Masiku amenewa musamadzagwire ntchito.+ Koma chakudya choti munthu aliyense adye, chimenecho chokha muzidzaphika.+

  • Ekisodo 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Muzidzadya mikate yosafufumitsa masiku 7,+ ndipo pa tsiku la 7 limenelo muzidzachita chikondwerero kwa Yehova.+

  • Levitiko 23:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kwa masiku 7, muzipereka kwa Yehova nsembe zotentha ndi moto. Pa tsiku la 7 muzichita msonkhano wopatulika ndipo musamagwire ntchito iliyonse yolemetsa.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena