Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Muzidya mkate wopanda chofufumitsa masiku 7. Tsiku loyamba muzichotsa m’nyumba zanu mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi chofufumitsa chifukwa aliyense wakudya mkate wokhala ndi chofufumitsa, kuchokera pa tsiku loyamba kukafika pa tsiku la 7,+ munthu wotero adzaphedwa kuti asakhalenso mu Isiraeli.+

  • Ekisodo 34:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Muzisunga chikondwerero cha mkate wosafufumitsa.+ Monga momwe ndinakulamulirani, muzidya mkate wosafufumitsa masiku 7 m’mwezi wa Abibu*+ pa nthawi yoikidwiratu, chifukwa munatuluka mu Iguputo m’mwezi wa Abibu.

  • 1 Akorinto 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chotero tiyeni tichite chikondwererochi,+ osati ndi chofufumitsa chakale,+ kapena chofufumitsa+ choimira zoipa ndi uchimo,+ koma ndi mikate yopanda chofufumitsa yoimira kuona mtima ndi choonadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena