Deuteronomo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kwa masiku 6, uzidya mkate wopanda chofufumitsa, ndipo pa tsiku la 7 uzichitira Yehova Mulungu wako+ msonkhano wapadera. Pa tsikuli usagwire ntchito.
8 Kwa masiku 6, uzidya mkate wopanda chofufumitsa, ndipo pa tsiku la 7 uzichitira Yehova Mulungu wako+ msonkhano wapadera. Pa tsikuli usagwire ntchito.