Numeri 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muziipereka pamodzi ndi nsembe yachakumwa+ chokwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini. Pa mwana wa nkhosa wamphongo+ aliyense muzipereka nsembe yachakumwa. Muzithirira Yehova nsembe yachakumwa choledzeretsayo+ m’malo oyera.
7 Muziipereka pamodzi ndi nsembe yachakumwa+ chokwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini. Pa mwana wa nkhosa wamphongo+ aliyense muzipereka nsembe yachakumwa. Muzithirira Yehova nsembe yachakumwa choledzeretsayo+ m’malo oyera.