Levitiko 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Isakhale yakhungu, yothyoka chiwalo, yotemeka, yokhala ndi njerewere, nkhanambo kapena zipere.+ Iliyonse yokhala ndi zimenezi musaipereke kwa Yehova ndipo musaike nsembe yotentha ndi moto+ ya nyama zoterezi paguwa lansembe la Yehova. Deuteronomo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Usapereke kwa Yehova Mulungu wako nsembe ya ng’ombe kapena nkhosa yokhala ndi chilema kapena vuto lililonse, chifukwa zimenezi ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wako.+
22 Isakhale yakhungu, yothyoka chiwalo, yotemeka, yokhala ndi njerewere, nkhanambo kapena zipere.+ Iliyonse yokhala ndi zimenezi musaipereke kwa Yehova ndipo musaike nsembe yotentha ndi moto+ ya nyama zoterezi paguwa lansembe la Yehova.
17 “Usapereke kwa Yehova Mulungu wako nsembe ya ng’ombe kapena nkhosa yokhala ndi chilema kapena vuto lililonse, chifukwa zimenezi ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wako.+